4 Koma mfumu ya Asuri inamva kuti Hoshiya akuikonzera chiwembu, chifukwa anatumiza anthu kwa So mfumu ya Iguputo+ ndiponso sanapereke msonkho kwa mfumu ya Asuri ngati mmene ankachitira zaka zamʼmbuyo. Choncho mfumu ya Asuri inamʼmanga nʼkumutsekera mʼndende.
7 “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Mfumu ya Yuda imene yakutumani kudzafunsira kwa ine mukaiuze kuti: “Taonani! Asilikali a Farao amene akubwera kudzakuthandizani adzabwerera kwawo ku Iguputo.+