Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 24:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Yehoyakini+ anayamba kulamulira ali ndi zaka 18 ndipo analamulira miyezi itatu ku Yerusalemu.+ Mayi ake anali a ku Yerusalemu ndipo dzina lawo linali Nehusita mwana wa Elinatani.

  • Yeremiya 24:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Kenako Yehova anandionetsa madengu awiri a nkhuyu amene anali patsogolo pa kachisi wa Yehova. Anandionetsa madenguwo pambuyo poti Nebukadinezara* mfumu ya Babulo watenga Yekoniya*+ mwana wa Yehoyakimu,+ mfumu ya Yuda, pamodzi ndi akalonga a Yuda, amisiri komanso anthu osula zitsulo,* kuchoka ku Yerusalemu nʼkupita nawo ku ukapolo ku Babulo.+

  • Yeremiya 37:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Ndiyeno Mfumu Zedekiya+ mwana wa Yosiya inayamba kulamulira mʼmalo mwa Koniya+ mwana wa Yehoyakimu chifukwa Mfumu Nebukadinezara* ya Babulo inamuika kuti akhale mfumu mʼdziko la Yuda.+

  • Mateyu 1:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Yosiya+ anabereka Yekoniya+ ndi azichimwene ake pa nthawi imene Ayuda anatengedwa kupita ku Babulo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena