Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 25:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Mkulu wa asilikali olondera mfumu uja anatenganso Seraya+ wansembe wamkulu, Zefaniya+ wansembe wachiwiri ndi alonda atatu apakhomo.+

  • 2 Mafumu 25:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Mfumu ya Babuloyo inapha anthuwo ku Ribila mʼdziko la Hamati.+ Choncho Ayuda anatengedwa kudziko lawo nʼkupita nawo ku ukapolo.+

  • Yeremiya 21:1, 2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Yeremiya analandira mawu ochokera kwa Yehova pamene Mfumu Zedekiya+ inatumiza Pasuri+ mwana wa Malikiya ndi Zefaniya+ mwana wa Maaseya, wansembe, kuti akamupemphe kuti: 2 “Chonde tifunsire kwa Yehova chifukwa Nebukadinezara,* mfumu ya ku Babulo, akufuna kuchita nafe nkhondo.+ Mwina Yehova atichitira imodzi mwa ntchito zake zodabwitsa moti Nebukadinezarayo atichokera.”+

  • Yeremiya 37:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndiyeno Mfumu Zedekiya inatuma Yehukali+ mwana wa Selemiya ndi Zefaniya+ mwana wa Maaseya wansembe kwa mneneri Yeremiya kukamuuza kuti: “Chonde, tipempherere kwa Yehova Mulungu wathu.”

  • Yeremiya 52:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Mkulu wa asilikali olondera mfumu uja anatenganso Seraya+ wansembe wamkulu, Zefaniya+ wansembe wachiwiri ndi alonda atatu apakhomo.+

  • Yeremiya 52:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Mfumu ya Babuloyo inapha anthuwo ku Ribila+ mʼdziko la Hamati. Choncho Ayuda anatengedwa kudziko lawo nʼkupita nawo ku ukapolo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena