Yesaya 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Sizidzavulazana+Kapena kuwonongana mʼphiri langa lonse loyera,+Chifukwa dziko lapansi lidzadzaza ndi anthu odziwa YehovaNgati mmene madzi amadzazira mʼnyanja.+ Habakuku 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chifukwa dziko lapansi lidzadzaza ndi anthu odziwa ulemerero wa Yehova,Ngati mmene madzi amadzazira nyanja.+
9 Sizidzavulazana+Kapena kuwonongana mʼphiri langa lonse loyera,+Chifukwa dziko lapansi lidzadzaza ndi anthu odziwa YehovaNgati mmene madzi amadzazira mʼnyanja.+
14 Chifukwa dziko lapansi lidzadzaza ndi anthu odziwa ulemerero wa Yehova,Ngati mmene madzi amadzazira nyanja.+