Salimo 51:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inu Mulungu, lengani mtima wolungama mkati mwanga,+Ndipo sinthani mmene ndimaganizira+ kuti ndikhale wokhulupirika. Ezekieli 36:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pa nthawiyo mudzakumbukira njira zanu zoipa ndi zochita zanu zimene sizinali zabwino. Mudzadzimvera chisoni chifukwa cha machimo anu komanso zinthu zonyansa zimene munkachita.+
10 Inu Mulungu, lengani mtima wolungama mkati mwanga,+Ndipo sinthani mmene ndimaganizira+ kuti ndikhale wokhulupirika.
31 Pa nthawiyo mudzakumbukira njira zanu zoipa ndi zochita zanu zimene sizinali zabwino. Mudzadzimvera chisoni chifukwa cha machimo anu komanso zinthu zonyansa zimene munkachita.+