Ezekieli 11:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndidzawapatsa mtima umodzi+ ndipo ndidzaika mzimu watsopano mwa iwo.+ Ndidzachotsa mtima wamwala mʼmatupi awo+ nʼkuwapatsa mtima wamnofu,*+ Aefeso 4:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndipo mupitirize kusintha kuti mukhale atsopano pa kaganizidwe kanu komanso mmene mumaonera zinthu.*+
19 Ndidzawapatsa mtima umodzi+ ndipo ndidzaika mzimu watsopano mwa iwo.+ Ndidzachotsa mtima wamwala mʼmatupi awo+ nʼkuwapatsa mtima wamnofu,*+
23 Ndipo mupitirize kusintha kuti mukhale atsopano pa kaganizidwe kanu komanso mmene mumaonera zinthu.*+