-
Ezekieli 30:10, 11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Ndidzawononga magulu a anthu a ku Iguputo pogwiritsa ntchito dzanja la Nebukadinezara,* mfumu ya Babulo.+ 11 Mfumuyo ndi asilikali ake, omwe ndi ankhanza kwambiri pa mayiko onse,+ adzabweretsedwa kuti adzawononge dzikolo. Iwo adzasolola malupanga awo nʼkuukira Iguputo ndipo adzadzaza dzikolo ndi anthu ophedwa.+
-
-
Habakuku 1:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Umene umathamanga mʼmadera ambiri apadziko lapansi,
Kukalanda nyumba zimene si zawo.+
-