Salimo 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yehova ndi Mfumu mpaka kalekale.+ Mitundu ya anthu yawonongedwa, yachotsedwa padziko lapansi.+ Danieli 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zizindikiro zake nʼzazikulu ndipo zochita zake nʼzamphamvu. Ufumu wake udzakhalapo mpaka kalekale ndipo ulamuliro wake udzakhalapo ku mibadwomibadwo.+
3 Zizindikiro zake nʼzazikulu ndipo zochita zake nʼzamphamvu. Ufumu wake udzakhalapo mpaka kalekale ndipo ulamuliro wake udzakhalapo ku mibadwomibadwo.+