Danieli 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno usiku, chinsinsicho chinaululidwa kwa Danieli mʼmasomphenya.+ Choncho Danieli anatamanda Mulungu wakumwamba. Danieli 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mʼchaka chachitatu cha ulamuliro wa Mfumu Belisazara,+ ineyo Danieli ndinaona masomphenya pambuyo pa masomphenya amene ndinaona poyamba aja.+
19 Ndiyeno usiku, chinsinsicho chinaululidwa kwa Danieli mʼmasomphenya.+ Choncho Danieli anatamanda Mulungu wakumwamba.
8 Mʼchaka chachitatu cha ulamuliro wa Mfumu Belisazara,+ ineyo Danieli ndinaona masomphenya pambuyo pa masomphenya amene ndinaona poyamba aja.+