Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Danieli 2:37, 38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Inuyo mfumu yomwe ndi mfumu ya mafumu, amene Mulungu wakumwamba wakupatsani ufumu,+ mphamvu ndi ulemerero, 38 inuyo amene Mulungu wakupatsani mphamvu zolamulira anthu kulikonse kumene akukhala komanso nyama zakutchire ndi mbalame zamumlengalenga, amene Mulungu wakuikani kuti muzilamulira zonsezi,+ inuyo ndi mutu wagolide.+

  • Danieli 7:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Chilombo choyamba chinali chooneka ngati mkango+ ndipo chinali ndi mapiko a chiwombankhanga.+ Ndinapitiriza kuchiyangʼana mpaka pamene mapiko ake anathotholedwa. Ndiyeno anachitukula panthaka nʼkuchiimiriritsa ndi miyendo iwiri ngati munthu. Kenako anachipatsa mtima wa munthu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena