Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 34:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndiyeno Yehova anadutsa pamaso pa Mose akulengeza kuti: “Yehova, Yehova, Mulungu wachifundo+ ndi wokoma mtima,*+ wosakwiya msanga+ ndiponso wachikondi chokhulupirika chochuluka+ komanso choonadi.*+

  • Salimo 78:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Koma ankawamvera chifundo.+

      Ankawakhululukira* machimo awo ndipo sankawawononga.+

      Nthawi zambiri ankabweza mkwiyo wake+

      Mʼmalo moonetsa ukali wake wonse.

  • Salimo 86:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Inu Yehova ndinu wabwino+ ndipo ndinu wokonzeka kukhululuka.+

      Mumasonyeza chikondi chokhulupirika chochuluka kwa onse amene amaitana inu.+

  • Salimo 145:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Yehova ndi wokoma mtima* komanso wachifundo,+

      Wosakwiya msanga ndiponso wodzaza ndi chikondi chokhulupirika.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena