Salimo 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mulungu wanga, Mulungu wanga, mwandisiyiranji ine?+ Nʼchifukwa chiyani mukuchedwa kundipulumutsa?Nʼchifukwa chiyani simukumva kubuula kwanga?+ Salimo 74:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inu Mulungu, kodi mdani adzapitiriza kunyoza mpaka liti?+ Kodi mdani adzachitira mwano dzina lanu mpaka kalekale?+ Chivumbulutso 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo anafuula ndi mawu okweza akuti: “Mudzalekerera mpaka liti, inu Ambuye Wamkulu Koposa, Mulungu woyera ndi woona,+ osaweruza ndi kubwezera okhala padziko lapansi chifukwa cha magazi athu?”+
22 Mulungu wanga, Mulungu wanga, mwandisiyiranji ine?+ Nʼchifukwa chiyani mukuchedwa kundipulumutsa?Nʼchifukwa chiyani simukumva kubuula kwanga?+
10 Inu Mulungu, kodi mdani adzapitiriza kunyoza mpaka liti?+ Kodi mdani adzachitira mwano dzina lanu mpaka kalekale?+
10 Iwo anafuula ndi mawu okweza akuti: “Mudzalekerera mpaka liti, inu Ambuye Wamkulu Koposa, Mulungu woyera ndi woona,+ osaweruza ndi kubwezera okhala padziko lapansi chifukwa cha magazi athu?”+