1 Timoteyo 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kwa Mulungu yekhayo+ yemwe ndi Mfumu yamuyaya,+ amene saafa+ komanso wosaoneka,+ kukhale ulemu ndi ulemerero mpaka kalekale. Ame. Chivumbulutso 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwo ankaimba nyimbo ya Mose+ kapolo wa Mulungu ndi nyimbo ya Mwanawankhosa+ yakuti: “Ntchito zanu nʼzazikulu ndi zodabwitsa,+ inu Yehova* Mulungu Wamphamvuyonse.+ Njira zanu ndi zolungama komanso zoona,+ inu Mfumu yamuyaya.+
17 Kwa Mulungu yekhayo+ yemwe ndi Mfumu yamuyaya,+ amene saafa+ komanso wosaoneka,+ kukhale ulemu ndi ulemerero mpaka kalekale. Ame.
3 Iwo ankaimba nyimbo ya Mose+ kapolo wa Mulungu ndi nyimbo ya Mwanawankhosa+ yakuti: “Ntchito zanu nʼzazikulu ndi zodabwitsa,+ inu Yehova* Mulungu Wamphamvuyonse.+ Njira zanu ndi zolungama komanso zoona,+ inu Mfumu yamuyaya.+