1 Mbiri 17:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ukadzamwalira nʼkugona mʼmanda ndi makolo ako, ndidzachititsa kuti mbadwa* yako, mmodzi wa ana ako,+ akhale mfumu ndipo ndidzachititsa kuti ufumu wake ukhazikike.+ Mateyu 9:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yesu akuchokera kumeneko, amuna awiri amene anali ndi vuto losaona+ anamutsatira akufuula kuti: “Mutichitire chifundo, Mwana wa Davide.” Luka 1:32, 33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ameneyu adzakhala wamkulu+ ndipo adzatchedwa Mwana wa Wamʼmwambamwamba.+ Yehova* Mulungu adzamupatsa mpando wachifumu wa Davide atate wake.+ 33 Iye adzalamulira monga Mfumu panyumba ya Yakobo kwamuyaya ndipo Ufumu wake sudzatha.”+
11 Ukadzamwalira nʼkugona mʼmanda ndi makolo ako, ndidzachititsa kuti mbadwa* yako, mmodzi wa ana ako,+ akhale mfumu ndipo ndidzachititsa kuti ufumu wake ukhazikike.+
27 Yesu akuchokera kumeneko, amuna awiri amene anali ndi vuto losaona+ anamutsatira akufuula kuti: “Mutichitire chifundo, Mwana wa Davide.”
32 Ameneyu adzakhala wamkulu+ ndipo adzatchedwa Mwana wa Wamʼmwambamwamba.+ Yehova* Mulungu adzamupatsa mpando wachifumu wa Davide atate wake.+ 33 Iye adzalamulira monga Mfumu panyumba ya Yakobo kwamuyaya ndipo Ufumu wake sudzatha.”+