Yesaya 55:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Inu nonse amene mukumva ludzu,+ bwerani mudzamwe madzi.+ Inu amene mulibe ndalama, bwerani mudzagule kuti mudye. Inde bwerani mudzagule vinyo ndi mkaka+ popanda ndalama ndiponso popanda mtengo.+ Luka 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Osangalala ndinu amene mukumva njala, chifukwa mudzakhuta.+ Osangalala ndinu amene mukulira, chifukwa mudzaseka.+
55 Inu nonse amene mukumva ludzu,+ bwerani mudzamwe madzi.+ Inu amene mulibe ndalama, bwerani mudzagule kuti mudye. Inde bwerani mudzagule vinyo ndi mkaka+ popanda ndalama ndiponso popanda mtengo.+
21 Osangalala ndinu amene mukumva njala, chifukwa mudzakhuta.+ Osangalala ndinu amene mukulira, chifukwa mudzaseka.+