-
Luka 11:2-4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Ndiyeno iye anawauza kuti: “Mukamapemphera muzinena kuti, ‘Atate, dzina lanu liyeretsedwe.*+ Ufumu wanu ubwere.+ 3 Mutipatse chakudya chalero mogwirizana ndi chakudya chofunika pa tsikuli.+ 4 Ndipo mutikhululukire machimo athu,+ chifukwa nafenso timakhululukira aliyense amene amatilakwira.*+ Komanso tithandizeni kuti tisagonje tikamayesedwa.’”*+
-