Mateyu 18:33, 34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Kodi sukanamuchitira chifundo kapolo mnzako, ngati mmene ine ndachitira kwa iwe?’+ 34 Choncho mbuye wakeyo anakwiya kwambiri ndipo anapita naye kwa oyangʼanira ndende kuti amutsekere mpaka atamaliza kubweza ngongole yonse ija. Yakobo 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chifukwa munthu amene sasonyeza chifundo adzaweruzidwa mopanda chifundo.+ Chifundo nʼchachikulu kuposa chiweruzo.
33 Kodi sukanamuchitira chifundo kapolo mnzako, ngati mmene ine ndachitira kwa iwe?’+ 34 Choncho mbuye wakeyo anakwiya kwambiri ndipo anapita naye kwa oyangʼanira ndende kuti amutsekere mpaka atamaliza kubweza ngongole yonse ija.
13 Chifukwa munthu amene sasonyeza chifundo adzaweruzidwa mopanda chifundo.+ Chifundo nʼchachikulu kuposa chiweruzo.