Yesaya 55:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Munthu woipa asiye njira yake+Ndipo wopweteka anzake asiye maganizo ake.Iye abwerere kwa Yehova ndipo adzamuchitira chifundo.+Abwerere kwa Mulungu wathu, chifukwa adzamukhululukira ndi mtima wonse.+ Mateyu 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mutikhululukire zolakwa* zathu chifukwa ifenso takhululukira amene atilakwira.*+ Mateyu 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho zinthu zonse zimene mukufuna kuti anthu akuchitireni, inunso muwachitire zomwezo.+ Zimenezi ndi zomwe Chilamulo chimafuna komanso zimene aneneri analemba.+ Yakobo 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chifukwa munthu amene sasonyeza chifundo adzaweruzidwa mopanda chifundo.+ Chifundo nʼchachikulu kuposa chiweruzo.
7 Munthu woipa asiye njira yake+Ndipo wopweteka anzake asiye maganizo ake.Iye abwerere kwa Yehova ndipo adzamuchitira chifundo.+Abwerere kwa Mulungu wathu, chifukwa adzamukhululukira ndi mtima wonse.+
12 Choncho zinthu zonse zimene mukufuna kuti anthu akuchitireni, inunso muwachitire zomwezo.+ Zimenezi ndi zomwe Chilamulo chimafuna komanso zimene aneneri analemba.+
13 Chifukwa munthu amene sasonyeza chifundo adzaweruzidwa mopanda chifundo.+ Chifundo nʼchachikulu kuposa chiweruzo.