Machitidwe 14:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mʼmalo onsewa ankalimbitsa ophunzira+ komanso kuwathandiza kuti apitirize kukhala ndi chikhulupiriro. Ankawauza kuti: “Tiyenera kukumana ndi mavuto ambiri kuti tikalowe mu Ufumu wa Mulungu.”+ 1 Petulo 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Ndipo ngati munthu wolungama angadzapulumuke movutikira, kodi chidzachitike nʼchiyani kwa munthu wosaopa Mulungu komanso wochimwa?”+
22 Mʼmalo onsewa ankalimbitsa ophunzira+ komanso kuwathandiza kuti apitirize kukhala ndi chikhulupiriro. Ankawauza kuti: “Tiyenera kukumana ndi mavuto ambiri kuti tikalowe mu Ufumu wa Mulungu.”+
18 “Ndipo ngati munthu wolungama angadzapulumuke movutikira, kodi chidzachitike nʼchiyani kwa munthu wosaopa Mulungu komanso wochimwa?”+