Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Maliko 3:14, 15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndiyeno anasankha gulu la anthu 12, amenenso anawapatsa dzina lakuti atumwi, kuti aziyenda naye nthawi zonse komanso kuti aziwatuma kukalalikira 15 nʼkuwapatsa mphamvu zoti azitulutsa ziwanda.+

  • Maliko 6:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Kenako anaitana ophunzira ake 12 aja nʼkuyamba kuwatumiza awiriawiri+ ndipo anawapatsa mphamvu kuti azitha kutulutsa mizimu yonyansa.+

  • Luka 9:1, 2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Kenako Yesu anasonkhanitsa atumwi 12 aja nʼkuwapatsa mphamvu ndi ulamuliro pa ziwanda zonse+ komanso kuti azitha kuchiritsa matenda.+ 2 Ndiyeno anawatumiza kuti azikalalikira za Ufumu wa Mulungu ndiponso kuchiritsa anthu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena