Mateyu 26:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Choncho atapita patsogolo pangʼono, anagwada mpaka nkhope yake pansi ndipo anapemphera kuti:+ “Atate wanga, ngati nʼkotheka lolani kuti kapu iyi+ indipitirire. Koma osati mwa kufuna kwanga, koma mwa kufuna kwanu.”+ Maliko 10:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Koma Yesu anawauza kuti: “Simukudziwa chimene mukupempha. Kodi mungamwe zimene ine ndikumwa kapena kubatizidwa ubatizo umene ine ndikubatizidwa?”+ Maliko 14:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Kenako anati: “Abba,* Atate,+ zinthu zonse nʼzotheka kwa inu. Ndichotsereni kapu iyi. Komatu osati mwa kufuna kwanga, koma mwa kufuna kwanu.”+ Yohane 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma Yesu anauza Petulo kuti: “Bwezera lupangalo mʼchimake.+ Kodi sindiyenera kumwa zamʼkapu imene Atate wandipatsa?”+
39 Choncho atapita patsogolo pangʼono, anagwada mpaka nkhope yake pansi ndipo anapemphera kuti:+ “Atate wanga, ngati nʼkotheka lolani kuti kapu iyi+ indipitirire. Koma osati mwa kufuna kwanga, koma mwa kufuna kwanu.”+
38 Koma Yesu anawauza kuti: “Simukudziwa chimene mukupempha. Kodi mungamwe zimene ine ndikumwa kapena kubatizidwa ubatizo umene ine ndikubatizidwa?”+
36 Kenako anati: “Abba,* Atate,+ zinthu zonse nʼzotheka kwa inu. Ndichotsereni kapu iyi. Komatu osati mwa kufuna kwanga, koma mwa kufuna kwanu.”+
11 Koma Yesu anauza Petulo kuti: “Bwezera lupangalo mʼchimake.+ Kodi sindiyenera kumwa zamʼkapu imene Atate wandipatsa?”+