Mateyu 20:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yesu anayankha kuti: “Simukudziwa chimene mukupempha. Kodi mungamwe zimene ine ndatsala pangʼono kumwa?”+ Iwo anayankha kuti: “Inde tingamwe.” Yohane 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma Yesu anauza Petulo kuti: “Bwezera lupangalo mʼchimake.+ Kodi sindiyenera kumwa zamʼkapu imene Atate wandipatsa?”+
22 Yesu anayankha kuti: “Simukudziwa chimene mukupempha. Kodi mungamwe zimene ine ndatsala pangʼono kumwa?”+ Iwo anayankha kuti: “Inde tingamwe.”
11 Koma Yesu anauza Petulo kuti: “Bwezera lupangalo mʼchimake.+ Kodi sindiyenera kumwa zamʼkapu imene Atate wandipatsa?”+