Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 16:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Kuyambira nthawi imeneyo, Yesu anayamba kuuza ophunzira ake kuti iyeyo akuyenera kupita ku Yerusalemu. Kumeneko akazunzidwa kwambiri ndi akulu, ansembe aakulu ndi alembi ndipo akaphedwa, koma pa tsiku lachitatu adzaukitsidwa.+

  • Mateyu 20:18, 19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 “Tsopano tikupita ku Yerusalemu ndipo Mwana wa munthu akaperekedwa kwa ansembe aakulu ndi alembi. Iwo akamuweruza kuti aphedwe+ 19 ndipo akamupereka kwa anthu a mitundu ina kuti amuchitire chipongwe, kumukwapula ndi kumupachika pamtengo+ ndipo pa tsiku lachitatu adzaukitsidwa.”+

  • Mateyu 27:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Choncho anawamasulira Baraba, koma analamula kuti Yesu akwapulidwe+ kenako anamupereka kuti akamuphe pomupachika pamtengo.+

  • Maliko 15:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Atatero, pofuna kukwaniritsa zofuna za anthuwo, Pilato anawamasulira Baraba. Ndiyeno analamula kuti Yesu akwapulidwe+ kenako anamupereka kuti akamuphe pomupachika pamtengo.+

  • Yohane 19:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Kenako anamupereka kwa iwo kuti akamuphe pomupachika pamtengo.+

      Tsopano Yesu anali mʼmanja mwawo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena