Maliko 14:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chifukwa osaukawo muli nawo nthawi zonse,+ ndipo mungathe kuwachitira zabwino nthawi iliyonse imene mwafuna. Koma ine simudzakhala nane nthawi zonse.+
7 Chifukwa osaukawo muli nawo nthawi zonse,+ ndipo mungathe kuwachitira zabwino nthawi iliyonse imene mwafuna. Koma ine simudzakhala nane nthawi zonse.+