Mateyu 26:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Osaukawo muli nawo nthawi zonse,+ koma ine simudzakhala nane nthawi zonse.+ Yohane 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Osaukawo muli nawo nthawi zonse,+ koma ine simudzakhala nane nthawi zonse.”+