Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Maliko 15:42, 43
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Tsopano popeza anali madzulo kwambiri komanso linali Tsiku Lokonzekera, kapena kuti tsiku loti mawa lake ndi Sabata, 43 kunabwera Yosefe wa ku Arimateya, munthu wodziwika wa mʼKhoti Lalikulu la Ayuda, amenenso ankayembekezera Ufumu wa Mulungu. Iye anapita molimba mtima kwa Pilato kukapempha mtembo wa Yesu.+

  • Luka 23:50-53
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 50 Ndiyeno panali mwamuna wina dzina lake Yosefe, amene anali wa mʼKhoti Lalikulu la Ayuda. Munthu ameneyu anali wabwino komanso wolungama.+ 51 (Iye sanavomereze chiwembu chawo komanso zimene anachita.) Yosefe anali wochokera ku Arimateya, mzinda wa Ayudeya ndipo ankayembekezera Ufumu wa Mulungu. 52 Iye anapita kwa Pilato kukapempha mtembo wa Yesu. 53 Choncho anautsitsa+ nʼkuukulunga munsalu yabwino kwambiri ndipo anakauika mʼmanda*+ amene anawagoba muthanthwe, mmene anali asanaikemo munthu chiyambire.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena