Yesaya 40:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Winawake akufuula mʼchipululu kuti: “Konzani njira ya Yehova!+ Mulungu wathu mukonzereni msewu wowongoka+ wodutsa mʼchipululu.+ Yohane 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iye anati: “Ndine mawu a winawake amene akufuula mʼchipululu kuti, ‘Wongolani njira ya Yehova,’*+ monga mmene mneneri Yesaya ananenera.”+
3 Winawake akufuula mʼchipululu kuti: “Konzani njira ya Yehova!+ Mulungu wathu mukonzereni msewu wowongoka+ wodutsa mʼchipululu.+
23 Iye anati: “Ndine mawu a winawake amene akufuula mʼchipululu kuti, ‘Wongolani njira ya Yehova,’*+ monga mmene mneneri Yesaya ananenera.”+