Salimo 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndifotokoza zimene Yehova wanena.Iye wandiuza kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga,+Lero, ine ndakhala bambo ako.+ Yesaya 42:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Taonani mtumiki wanga+ amene ndikumuthandiza, Wosankhidwa wanga+ amene amandisangalatsa,+ Ine ndaika mzimu wanga mwa iye.+Iye adzabweretsa chilungamo kwa anthu a mitundu ina.+ Mateyu 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Panamvekanso mawu ochokera kumwamba+ onena kuti: “Uyu ndi Mwana wanga+ wokondedwa ndipo amandisangalatsa kwambiri.”+ 2 Petulo 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chifukwa Khristu analandira ulemu ndi ulemerero kuchokera kwa Mulungu, Atate wathu, pamene mawu anamveka kwa iye kuchokera mu ulemerero waukulu kuti: “Uyu ndi Mwana wanga wokondedwa, amene amandisangalatsa kwambiri.”+
7 Ndifotokoza zimene Yehova wanena.Iye wandiuza kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga,+Lero, ine ndakhala bambo ako.+
42 Taonani mtumiki wanga+ amene ndikumuthandiza, Wosankhidwa wanga+ amene amandisangalatsa,+ Ine ndaika mzimu wanga mwa iye.+Iye adzabweretsa chilungamo kwa anthu a mitundu ina.+
17 Panamvekanso mawu ochokera kumwamba+ onena kuti: “Uyu ndi Mwana wanga+ wokondedwa ndipo amandisangalatsa kwambiri.”+
17 Chifukwa Khristu analandira ulemu ndi ulemerero kuchokera kwa Mulungu, Atate wathu, pamene mawu anamveka kwa iye kuchokera mu ulemerero waukulu kuti: “Uyu ndi Mwana wanga wokondedwa, amene amandisangalatsa kwambiri.”+