Salimo 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndifotokoza zimene Yehova wanena.Iye wandiuza kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga,+Lero, ine ndakhala bambo ako.+ Mateyu 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Patapita masiku 6, Yesu anatenga Petulo, Yakobo ndi mchimwene wake Yohane nʼkukwera nawo mʼphiri lalitali kwaokhaokha.+ Mateyu 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mawu ake adakali mʼkamwa, mtambo wowala kwambiri unawaphimba ndipo panamveka mawu kuchokera mumtambomo akuti: “Uyu ndi Mwana wanga wokondedwa, amene amandisangalatsa kwambiri.+ Muzimumvera.”+ Maliko 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno kunachita mtambo umene unawaphimba. Kenako panamveka mawu+ kuchokera mumtambomo akuti: “Uyu ndi Mwana wanga wokondedwa.+ Muzimumvera.”+ Luka 9:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Ndiyeno panamveka mawu+ kuchokera mumtambomo akuti: “Uyu ndi Mwana wanga, amene ndinamusankha.+ Muzimumvera.”+
7 Ndifotokoza zimene Yehova wanena.Iye wandiuza kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga,+Lero, ine ndakhala bambo ako.+
17 Patapita masiku 6, Yesu anatenga Petulo, Yakobo ndi mchimwene wake Yohane nʼkukwera nawo mʼphiri lalitali kwaokhaokha.+
5 Mawu ake adakali mʼkamwa, mtambo wowala kwambiri unawaphimba ndipo panamveka mawu kuchokera mumtambomo akuti: “Uyu ndi Mwana wanga wokondedwa, amene amandisangalatsa kwambiri.+ Muzimumvera.”+
7 Ndiyeno kunachita mtambo umene unawaphimba. Kenako panamveka mawu+ kuchokera mumtambomo akuti: “Uyu ndi Mwana wanga wokondedwa.+ Muzimumvera.”+
35 Ndiyeno panamveka mawu+ kuchokera mumtambomo akuti: “Uyu ndi Mwana wanga, amene ndinamusankha.+ Muzimumvera.”+