Mateyu 26:57 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Anthu amene anagwira Yesu aja anapita naye kwa Kayafa+ mkulu wa ansembe, kumene alembi ndi akulu anali atasonkhana.+ Luka 22:54, 55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Zitatero anamugwira nʼkumutenga+ ndipo anakamulowetsa mʼnyumba ya mkulu wa ansembe. Koma Petulo ankawatsatira chapatali.+ 55 Atasonkha moto mkati mwa bwalo nʼkukhala pansi onse pamodzi, Petulo nayenso anakhala nawo pamenepo.+
57 Anthu amene anagwira Yesu aja anapita naye kwa Kayafa+ mkulu wa ansembe, kumene alembi ndi akulu anali atasonkhana.+
54 Zitatero anamugwira nʼkumutenga+ ndipo anakamulowetsa mʼnyumba ya mkulu wa ansembe. Koma Petulo ankawatsatira chapatali.+ 55 Atasonkha moto mkati mwa bwalo nʼkukhala pansi onse pamodzi, Petulo nayenso anakhala nawo pamenepo.+