Luka 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yohane anayankha onsewo kuti: “Ine ndikukubatizani ndi madzi. Koma wina wamphamvu kuposa ine akubwera, amene ine sindili woyenera kumasula zingwe za nsapato zake.+ Iyeyu adzakubatizani ndi mzimu woyera komanso moto.+ Yohane 1:26, 27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Yohane anawayankha kuti: “Ine ndimabatiza mʼmadzi. Pakati panu paimirira wina amene inu simukumudziwa. 27 Iye ndi amene akubwera mʼmbuyo mwangamu ndipo ine si woyenera kumasula zingwe za nsapato zake.”+ Machitidwe 13:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma pamene Yohane ankamaliza utumiki wake, ankanena kuti, ‘Kodi mukuganiza kuti ndine ndani? Amene mukumuganizirayo si ine ayi. Koma wina akubwera pambuyo panga, amene ine si woyenera kumasula nsapato zake.’+
16 Yohane anayankha onsewo kuti: “Ine ndikukubatizani ndi madzi. Koma wina wamphamvu kuposa ine akubwera, amene ine sindili woyenera kumasula zingwe za nsapato zake.+ Iyeyu adzakubatizani ndi mzimu woyera komanso moto.+
26 Yohane anawayankha kuti: “Ine ndimabatiza mʼmadzi. Pakati panu paimirira wina amene inu simukumudziwa. 27 Iye ndi amene akubwera mʼmbuyo mwangamu ndipo ine si woyenera kumasula zingwe za nsapato zake.”+
25 Koma pamene Yohane ankamaliza utumiki wake, ankanena kuti, ‘Kodi mukuganiza kuti ndine ndani? Amene mukumuganizirayo si ine ayi. Koma wina akubwera pambuyo panga, amene ine si woyenera kumasula nsapato zake.’+