Luka 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yohane anawayankha onsewo kuti: “Inetu ndikukubatizani m’madzi. Koma wina wamphamvu kuposa ine akubwera, amene ine sindili woyenera kumasula zingwe za nsapato zake.+ Iyeyu adzakubatizani ndi mzimu woyera ndi moto.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:16 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, article 110 Nsanja ya Olonda,5/15/1995, tsa. 30
16 Yohane anawayankha onsewo kuti: “Inetu ndikukubatizani m’madzi. Koma wina wamphamvu kuposa ine akubwera, amene ine sindili woyenera kumasula zingwe za nsapato zake.+ Iyeyu adzakubatizani ndi mzimu woyera ndi moto.+