Mateyu 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Atabatizidwa, nthawi yomweyo Yesu anavuuka mʼmadzimo. Pamenepo kumwamba kunatseguka,+ ndipo Yohane anaona mzimu wa Mulungu ukutsika ngati nkhunda nʼkudzamutera.+ Maliko 1:9, 10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mʼmasiku amenewo, Yesu anabwera kuchokera ku Nazareti wa ku Galileya ndipo anabatizidwa ndi Yohane mu Yorodano.+ 10 Atangovuuka mʼmadzimo, iye anaona kumwamba kukutseguka ndiponso mzimu ukutsika ngati nkhunda kudzamutera.+
16 Atabatizidwa, nthawi yomweyo Yesu anavuuka mʼmadzimo. Pamenepo kumwamba kunatseguka,+ ndipo Yohane anaona mzimu wa Mulungu ukutsika ngati nkhunda nʼkudzamutera.+
9 Mʼmasiku amenewo, Yesu anabwera kuchokera ku Nazareti wa ku Galileya ndipo anabatizidwa ndi Yohane mu Yorodano.+ 10 Atangovuuka mʼmadzimo, iye anaona kumwamba kukutseguka ndiponso mzimu ukutsika ngati nkhunda kudzamutera.+