Salimo 45:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiwe wokongola kwambiri pakati pa ana a anthu. Mʼkamwa mwako mumatuluka mawu osangalatsa.+ Nʼchifukwa chake Mulungu wakudalitsa mpaka kalekale.+ Yesaya 50:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wandipatsa lilime la anthu ophunzitsidwa bwino*+Kuti ndidziwe mmene ndingayankhire* munthu amene watopa, ndi mawu oyenera.+ Iye amandidzutsa mʼmawa uliwonse.Amandidzutsa kuti ndimvetsere* ngati mmene ophunzira amachitira.+
2 Ndiwe wokongola kwambiri pakati pa ana a anthu. Mʼkamwa mwako mumatuluka mawu osangalatsa.+ Nʼchifukwa chake Mulungu wakudalitsa mpaka kalekale.+
4 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wandipatsa lilime la anthu ophunzitsidwa bwino*+Kuti ndidziwe mmene ndingayankhire* munthu amene watopa, ndi mawu oyenera.+ Iye amandidzutsa mʼmawa uliwonse.Amandidzutsa kuti ndimvetsere* ngati mmene ophunzira amachitira.+