Mateyu 5:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Choncho khalani angwiro,* mofanana ndi Atate wanu wakumwamba amene ndi wangwiro.”+ Aefeso 5:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho muzitsanzira Mulungu,+ monga ana ake okondedwa, 2 ndipo pitirizani kusonyeza chikondi+ ngati mmene Khristu anatikondera*+ nʼkudzipereka yekha chifukwa cha ife* ngati chopereka ndiponso ngati nsembe yafungo lokoma kwa Mulungu.+ Yakobo 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chifukwa munthu amene sasonyeza chifundo adzaweruzidwa mopanda chifundo.+ Chifundo nʼchachikulu kuposa chiweruzo.
5 Choncho muzitsanzira Mulungu,+ monga ana ake okondedwa, 2 ndipo pitirizani kusonyeza chikondi+ ngati mmene Khristu anatikondera*+ nʼkudzipereka yekha chifukwa cha ife* ngati chopereka ndiponso ngati nsembe yafungo lokoma kwa Mulungu.+
13 Chifukwa munthu amene sasonyeza chifundo adzaweruzidwa mopanda chifundo.+ Chifundo nʼchachikulu kuposa chiweruzo.