Mateyu 5:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Choncho khalani angwiro,* mofanana ndi Atate wanu wakumwamba amene ndi wangwiro.”+ Luka 6:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Pitirizani kukhala achifundo, mofanana ndi Atate wanu amenenso ndi wachifundo.+