Mateyu 7:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Siyani kuweruza ena+ kuti inunso musaweruzidwe, 2 chifukwa mmene mumaweruzira ena inunso adzakuweruzani choncho.+ Ndipo muyezo umene mukuyezera ena iwonso adzakuyezerani womwewo.+ Aroma 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nanga nʼchifukwa chiyani umaweruza mʼbale wako?+ Kapenanso nʼchifukwa chiyani umanyoza mʼbale wako? Popeza tonse tidzaima patsogolo pa mpando woweruzira wa Mulungu.+
7 “Siyani kuweruza ena+ kuti inunso musaweruzidwe, 2 chifukwa mmene mumaweruzira ena inunso adzakuweruzani choncho.+ Ndipo muyezo umene mukuyezera ena iwonso adzakuyezerani womwewo.+
10 Nanga nʼchifukwa chiyani umaweruza mʼbale wako?+ Kapenanso nʼchifukwa chiyani umanyoza mʼbale wako? Popeza tonse tidzaima patsogolo pa mpando woweruzira wa Mulungu.+