Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 27:41-43
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 41 Chimodzimodzinso ansembe aakulu limodzi ndi alembi komanso akulu. Nawonso anayamba kumunyoza nʼkumanena kuti:+ 42 “Ena anatha kuwapulumutsa, koma kuti adzipulumutse yekha zikumukanika! Ngati ali Mfumu ya Isiraeli,+ tiyeni tione ngati angatsike pamtengo wozunzikirapowo* ndipo ife timukhulupirira. 43 Paja iye amakhulupirira Mulungu, ndiye panopa Mulunguyo amupulumutse ngati akumufunadi+ chifukwa iye ankanena kuti, ‘Ine ndine Mwana wa Mulungu.’”+

  • Luka 23:35, 36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Anthu anangoima nʼkumaonerera zimene zinkachitikazo. Koma olamulira ankamunyogodola nʼkumanena kuti: “Ena anatha kuwapulumutsa, musiyeni adzipulumutse yekha, ngati alidi Khristu wa Mulungu, Wosankhidwa.”+ 36 Ngakhale asilikali nawonso ankamuchitira zachipongwe, ankabwera kudzamupatsa vinyo wowawasa+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena