Mateyu 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mʼmasiku amenewo, Yohane+ Mʼbatizi anapita mʼchipululu cha Yudeya nʼkuyamba kulalikira.+ Luka 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mʼmasiku amenewo Anasi anali wansembe wamkulu ndipo Kayafa+ anali mkulu wa ansembe. Pa nthawiyo mawu a Mulungu anafika kwa Yohane+ mwana wa Zekariya mʼchipululu.+
2 Mʼmasiku amenewo Anasi anali wansembe wamkulu ndipo Kayafa+ anali mkulu wa ansembe. Pa nthawiyo mawu a Mulungu anafika kwa Yohane+ mwana wa Zekariya mʼchipululu.+