Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 53:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Chifukwa cha kuvutika kwake, iye adzaona zabwino ndipo adzakhutira.

      Chifukwa cha zimene mtumiki wanga wolungama akudziwa,+

      Adzachititsa kuti anthu ambiri azionedwa olungama,+

      Ndipo adzanyamula zolakwa zawo.+

  • Aroma 3:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Taona kuti munthu amakhala wolungama mwa chikhulupiriro, osati potsatira Chilamulo.+

  • Aroma 5:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Choncho, mmene zinakhalira kuti uchimo umodzi unachititsa kuti anthu osiyanasiyana aweruzidwe kuti ndi ochimwa,+ kuchita chinthu chimodzi cholungama kwachititsanso kuti anthu osiyanasiyana+ aonedwe kuti ndi olungama kuti akhale ndi moyo.+

  • Aroma 8:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Chilamulo chinalibe mphamvu yokumasulani+ chifukwa anthu ndi ofooka+ komanso ochimwa. Koma kuti akumasuleni, Mulungu anatumiza Mwana wake+ ali ndi thupi ngati la anthu ochimwa+ kuti athane ndi uchimo. Choncho Mulungu anagonjetsa uchimo pogwiritsa ntchito thupi.

  • Aheberi 7:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Chilamulo sichinapangitse chilichonse kukhala changwiro.+ Koma chiyembekezo cha zinthu zabwino chimene anabweretsa,+ chomwe chikutithandiza kuyandikira Mulungu,+ chinachita zimenezi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena