Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 3:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Munapha Mtumiki Wamkulu wa moyo,+ koma Mulungu anamuukitsa ndipo ife ndife mboni za nkhani imeneyi.+

  • Aroma 4:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Analemberanso ifeyo. Nafenso timaonedwa kuti ndife olungama chifukwa timakhulupirira Mulungu amene anaukitsa Yesu Ambuye wathu.+

  • 1 Akorinto 6:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Koma Mulungu anaukitsa Ambuye+ ndipo adzaukitsanso ifeyo+ pogwiritsa ntchito mphamvu zake.+

  • Akolose 2:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Zili choncho chifukwa munaikidwa naye limodzi mʼmanda pobatizidwa ubatizo wofanana ndi wake.+ Ndipo popeza muli naye pa ubwenzi komanso mumakhulupirira zinthu zimene Mulungu, amene anamuukitsa kwa akufa+ anapanga ndi mphamvu zake, munaukitsidwa naye limodzi.+

  • Aheberi 13:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Tsopano, Mulungu wamtendere amene anaukitsa mʼbusa wamkulu+ wa nkhosa amene ali ndi magazi a pangano losatha, Ambuye wathu Yesu,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena