-
Mateyu 28:19, 20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Choncho pitani mukaphunzitse anthu a mitundu yonse kuti akhale ophunzira anga.+ Muziwabatiza+ mʼdzina la Atate, la Mwana ndi la mzimu woyera, 20 ndipo muziwaphunzitsa kuti azisunga zinthu zonse zimene ndinakulamulani.+ Ndipo dziwani kuti ine ndili limodzi ndi inu masiku onse mpaka mʼnyengo ya mapeto a nthawi* ino.”+
-