1 Akorinto 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho ngati chakudya chikukhumudwitsa mʼbale wanga, sindidzadyanso nyama ngakhale pangʼono, kuti ndisakhumudwitse mʼbale wanga.+ 1 Akorinto 13:4, 5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chikondi+ nʼcholeza mtima+ ndiponso nʼchokoma mtima.+ Chikondi sichichita nsanje,+ sichidzitama, sichidzikuza,+ 5 sichichita zosayenera,*+ sichisamala zofuna zake zokha,+ sichikwiya+ ndipo sichisunga zifukwa.+
13 Choncho ngati chakudya chikukhumudwitsa mʼbale wanga, sindidzadyanso nyama ngakhale pangʼono, kuti ndisakhumudwitse mʼbale wanga.+
4 Chikondi+ nʼcholeza mtima+ ndiponso nʼchokoma mtima.+ Chikondi sichichita nsanje,+ sichidzitama, sichidzikuza,+ 5 sichichita zosayenera,*+ sichisamala zofuna zake zokha,+ sichikwiya+ ndipo sichisunga zifukwa.+