Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 26:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Akupitiriza kudya, Yesu anatenga mkate ndipo atayamika Mulungu, anaunyemanyema+ nʼkuupereka kwa ophunzira ake. Iye ananena kuti: “Eni, idyani. Mkate uwu ukuimira thupi langa.”+

  • Maliko 14:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Akupitiriza kudya, iye anatenga mkate nʼkuyamika Mulungu. Kenako anaunyemanyema nʼkuwapatsa ndipo anati: “Tengani, mkate uwu ukuimira thupi langa.”+

  • Aroma 7:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Abale anga, thupi la Khristu linakumasulani ku Chilamulo, kuti mukhale a winawake+ amene anaukitsidwa+ nʼcholinga choti tibale zipatso kwa Mulungu.+

  • 1 Akorinto 10:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Popeza pali mkate umodzi, ifeyo, ngakhale kuti tilipo ambiri, ndife thupi limodzi,+ chifukwa tonse tikudya nawo mkate umodziwo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena