Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Maliko 14:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Akupitiriza kudya, iye anatenga mkate nʼkuyamika Mulungu. Kenako anaunyemanyema nʼkuwapatsa ndipo anati: “Tengani, mkate uwu ukuimira thupi langa.”+

  • Luka 22:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Kenako anatenga mkate.+ Atayamika, anaunyemanyema nʼkuwapatsa ndipo anati: “Mkate uwu ukuimira thupi langa+ limene likuperekedwa chifukwa cha inu.+ Muzichita zimenezi pondikumbukira.”+

  • 1 Akorinto 11:23-26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Zimene ndinamva kwa Ambuye nʼzimene inenso ndinakuphunzitsani, kuti Ambuye Yesu, usiku+ umene anaperekedwa anatenga mkate, 24 ndipo atayamika anaugawagawa* nʼkunena kuti: “Mkate uwu ukuimira thupi langa+ limene likuperekedwa chifukwa cha inu. Muzichita zimenezi pondikumbukira.”+ 25 Anachitanso chimodzimodzi ndi kapu+ atadya chakudya chamadzulo, ndipo anati: “Kapu iyi ikuimira pangano latsopano+ limene linakhazikitsidwa pogwiritsa ntchito magazi anga.+ Muzichita zimenezi mukamamwa zamʼkapu imeneyi pondikumbukira.”+ 26 Chifukwa nthawi iliyonse imene mukudya mkate umenewu ndi kumwa zamʼkapu imeneyi, mumakhala kuti mukulengeza imfa ya Ambuye, mpaka iye adzabwere.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena