Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 16:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndiyeno muzichitira Yehova Mulungu wanu Chikondwerero cha Masabata,+ popereka nsembe zaufulu zimene mungathe, mogwirizana ndi mmene Yehova Mulungu wanu wakudalitsirani.+

  • Deuteronomo 16:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Mphatso imene aliyense ayenera kubweretsa izikhala yogwirizana ndi madalitso amene Yehova Mulungu wanu wakupatsani.+

  • Miyambo 3:27, 28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Usalephere kuchitira zabwino anthu amene ukuyenera kuwachitira* zabwinozo,+

      Ngati ungathe kuwathandiza.*+

      28 Mnzako usamuuze kuti, “Pita, ukabwerenso mawa ndipo ndidzakupatsa,”

      Ngati ungathe kumupatsa nthawi yomweyo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena