Salimo 34:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mngelo wa Yehova amamanga msasa kuzungulira anthu onse amene amaopa Mulungu,+Ndipo amawapulumutsa.+ Salimo 91:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa adzalamula angelo ake+ zokhudza iwe,Kuti akuteteze mʼnjira zako zonse.+ Machitidwe 5:18, 19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 nʼkugwira atumwiwo ndipo anawatsekera mʼndende.+ 19 Koma usiku, mngelo wa Yehova* anatsegula zitseko za ndendeyo nʼkuwatulutsa,+ ndipo anawauza kuti:
7 Mngelo wa Yehova amamanga msasa kuzungulira anthu onse amene amaopa Mulungu,+Ndipo amawapulumutsa.+
18 nʼkugwira atumwiwo ndipo anawatsekera mʼndende.+ 19 Koma usiku, mngelo wa Yehova* anatsegula zitseko za ndendeyo nʼkuwatulutsa,+ ndipo anawauza kuti: