2 Akorinto 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chiyembekezo chathu pa inu sichikugwedezeka, chifukwa tikudziwa kuti popeza mukukumana ndi mavuto ofanana ndi amene ifeyo tikukumana nawo, nanunso mudzatonthozedwa.+ Akolose 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Tsopano ndikusangalala ndi mavuto amene ndikukumana nawo chifukwa cha inu.+ Ndipo inenso ndikuona kuti sindinazunzikebe mokwanira monga chiwalo cha thupi la Khristu,+ limene ndi mpingo.+
7 Chiyembekezo chathu pa inu sichikugwedezeka, chifukwa tikudziwa kuti popeza mukukumana ndi mavuto ofanana ndi amene ifeyo tikukumana nawo, nanunso mudzatonthozedwa.+
24 Tsopano ndikusangalala ndi mavuto amene ndikukumana nawo chifukwa cha inu.+ Ndipo inenso ndikuona kuti sindinazunzikebe mokwanira monga chiwalo cha thupi la Khristu,+ limene ndi mpingo.+