Miyambo 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chidani nʼchimene chimayambitsa mikangano,Koma chikondi chimaphimba machimo onse.+ Miyambo 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Aliyense amene amakhululuka* zolakwa akufunafuna chikondi,+Koma amene amangokhalira kulankhula za nkhani inayake amalekanitsa mabwenzi apamtima.+ 1 Akorinto 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chikondi+ nʼcholeza mtima+ ndiponso nʼchokoma mtima.+ Chikondi sichichita nsanje,+ sichidzitama, sichidzikuza,+ 1 Akorinto 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chimakwirira zinthu zonse,+ chimakhulupirira zinthu zonse,+ chimayembekezera zinthu zonse+ komanso chimapirira zinthu zonse.+
9 Aliyense amene amakhululuka* zolakwa akufunafuna chikondi,+Koma amene amangokhalira kulankhula za nkhani inayake amalekanitsa mabwenzi apamtima.+
4 Chikondi+ nʼcholeza mtima+ ndiponso nʼchokoma mtima.+ Chikondi sichichita nsanje,+ sichidzitama, sichidzikuza,+
7 Chimakwirira zinthu zonse,+ chimakhulupirira zinthu zonse,+ chimayembekezera zinthu zonse+ komanso chimapirira zinthu zonse.+