Yesaya 65:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Taonani! Ndikulenga kumwamba kwatsopano ndi dziko lapansi latsopano.+Ndipo zinthu zakale sizidzakumbukiridwanso,Kapena kuvutitsa maganizo.+ Yesaya 66:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Chifukwa kumwamba kwatsopano ndi dziko lapansi latsopano+ zimene ndikupanga zidzapitiriza kukhala pamaso panga. Mofanana ndi zimenezi, ana anu* ndi dzina lanu zidzapitiriza kukhalapo,”+ akutero Yehova. Chivumbulutso 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno ndinaona kumwamba kwatsopano ndi dziko lapansi latsopano,+ chifukwa kumwamba kwakale ndi dziko lapansi lakale zinali zitachoka+ ndipo kulibenso nyanja.+
17 Taonani! Ndikulenga kumwamba kwatsopano ndi dziko lapansi latsopano.+Ndipo zinthu zakale sizidzakumbukiridwanso,Kapena kuvutitsa maganizo.+
22 “Chifukwa kumwamba kwatsopano ndi dziko lapansi latsopano+ zimene ndikupanga zidzapitiriza kukhala pamaso panga. Mofanana ndi zimenezi, ana anu* ndi dzina lanu zidzapitiriza kukhalapo,”+ akutero Yehova.
21 Ndiyeno ndinaona kumwamba kwatsopano ndi dziko lapansi latsopano,+ chifukwa kumwamba kwakale ndi dziko lapansi lakale zinali zitachoka+ ndipo kulibenso nyanja.+